Search Badges Account

How does little girl get ready for school?

Pamene anali mtsikana wamng’ono Zanele Situ anauzidwa kuti sadzayendnso. Kukhala mu mphando wa mawilo sikunamletse. Anagwira nchito yaikulu ndi kuphunzira molimbika ndi kupambana za masewero a dziko. Iyi ndi nkhani yake…

Atate ake Neo amapanga zopangapanga. Pamene anapanga chisoti chobvala mundege yosathamanga ponyamuka ndi ku uluka, Neo anaganiza kupanga chopanga chake chake.

Do you know all your body parts? Find out!

Konzekani, khazikikani, pitani… phunzirani sayansi ya kusewera.

Banja la Thabo liri kukonzekera zochitika mtsiku ndipo zinthu ziri mbwembwembwe pamene alikukonzekera. Nanga Thabo alikuti?

Musuku anakolola zambiri kucoka m’munda ndipo anaika zokolola zake munkokwe. Anaika tanje wamkulu pamwamba kuti abise zonse zomwe zinali mnkokwe ndi kulemba cona nchito yokhala malonda. Tanje uyu anali wamkulu womwe sauonepo m’mudzi wa Musuku. Ambiri anakhala ndi cidwi ndi tanje uyu maka-maka nyani omwe anali mbala. Kodi muganiza kuti cona azateteza tanje ndi zokolola zina zonse?

Amai apita pakamphindi kang’ono. Kodi ndi chiyani chingachitike?

Hamisi goes to buy his uniform and spots a shirt he wants. His father says he doesn’t have the money for it. What will happen to Hamisi’s wish?

Mnyumba mwa Savana muli zii. Kodi angathe kuchita chiyani kuti mumveke mimvekero? Wayamba kupanga nyimbo zake. Tiyeni timvetsere.