Dotolo wa Thonje
Margaret anali wofunitsitsa kudziwa zinthu. Margaret anali ndi maloto akulu. Koma zaka 200 zitapita, mtsikana sanali kuloledwa kukhal dotolo. Teo anameta tsitsi lake ndi kubvala zobzala za munthu wa mwamuna. Kuchokera pamenepo, anthu sanadziwe kuti Margaret ndi munthu wachimai. Anakhala James Barry.